Chivumbulutso 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chotero ndinatenga mpukutu waung’onowo m’dzanja la mngeloyo n’kuudya.+ M’kamwa mwanga, unali wozuna ngati uchi,+ koma nditaudya, unandipweteketsa m’mimba. Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:10 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 158-160 Nsanja ya Olonda,12/15/1988, tsa. 1310/15/1988, tsa. 14
10 Chotero ndinatenga mpukutu waung’onowo m’dzanja la mngeloyo n’kuudya.+ M’kamwa mwanga, unali wozuna ngati uchi,+ koma nditaudya, unandipweteketsa m’mimba.