Salimo 119:103 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 103 Mawu anu amatsekemera m’kamwa mwanga,Kuposa mmene uchi umakomera!+ Ezekieli 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, idya mpukutu umene ndikukupatsawu, kuti mimba yako ikhute ndiponso kuti mpukutuwo udzaze m’matumbo mwako.” Choncho ndinayamba kudya mpukutuwo, ndipo unali wotsekemera* ngati uchi m’kamwa mwanga.+
3 Kenako anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, idya mpukutu umene ndikukupatsawu, kuti mimba yako ikhute ndiponso kuti mpukutuwo udzaze m’matumbo mwako.” Choncho ndinayamba kudya mpukutuwo, ndipo unali wotsekemera* ngati uchi m’kamwa mwanga.+