Salimo 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 N’zolakalakika kuposa golide, kuposa golide wambiri woyengeka bwino.+N’zotsekemera* kuposa uchi,+ inde kuposa uchi umene ukukha m’zisa.+ Salimo 119:103 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 103 Mawu anu amatsekemera m’kamwa mwanga,Kuposa mmene uchi umakomera!+ Yeremiya 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mawu anu anandipeza ndipo ndinawadya.+ Mawu anu amandikondweretsa+ ndi kusangalatsa mtima wanga,+ pakuti ine ndimatchedwa ndi dzina lanu,+ inu Yehova Mulungu wa makamu.+ Chivumbulutso 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho, ndinapita kwa mngeloyo n’kumuuza kuti andipatse mpukutu waung’onowo. Iye anandiuza kuti: “Tenga mpukutuwu udye.+ Ukupweteketsa m’mimba, koma m’kamwa mwako ukhala wozuna ngati uchi.”
10 N’zolakalakika kuposa golide, kuposa golide wambiri woyengeka bwino.+N’zotsekemera* kuposa uchi,+ inde kuposa uchi umene ukukha m’zisa.+
16 Mawu anu anandipeza ndipo ndinawadya.+ Mawu anu amandikondweretsa+ ndi kusangalatsa mtima wanga,+ pakuti ine ndimatchedwa ndi dzina lanu,+ inu Yehova Mulungu wa makamu.+
9 Choncho, ndinapita kwa mngeloyo n’kumuuza kuti andipatse mpukutu waung’onowo. Iye anandiuza kuti: “Tenga mpukutuwu udye.+ Ukupweteketsa m’mimba, koma m’kamwa mwako ukhala wozuna ngati uchi.”