Ezekieli 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Iwe mwana wa munthu, imva zimene ndikukuuza. Usapanduke ngati nyumba yopandukayi.+ Tsegula pakamwa pako kuti udye zimene ndikukupatsa.”+
8 “Iwe mwana wa munthu, imva zimene ndikukuuza. Usapanduke ngati nyumba yopandukayi.+ Tsegula pakamwa pako kuti udye zimene ndikukupatsa.”+