Numeri 20:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Aroni aikidwe m’manda, agone ndi makolo ake,+ pakuti sadzalowa m’dziko limene ndidzapatse ana a Isiraeli. Izi zili choncho chifukwa amuna inu munapandukira malangizo anga okhudza madzi a ku Meriba.+ Yesaya 50:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanditsegula khutu ndipo ineyo sindinapanduke.+ Sindinatembenukire kwina.+
24 “Aroni aikidwe m’manda, agone ndi makolo ake,+ pakuti sadzalowa m’dziko limene ndidzapatse ana a Isiraeli. Izi zili choncho chifukwa amuna inu munapandukira malangizo anga okhudza madzi a ku Meriba.+
5 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanditsegula khutu ndipo ineyo sindinapanduke.+ Sindinatembenukire kwina.+