Ezekieli 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Iwe mwana wa munthu, imva zimene ndikukuuza. Usapanduke ngati nyumba yopandukayi.+ Tsegula pakamwa pako kuti udye zimene ndikukupatsa.”+ Chivumbulutso 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho, ndinapita kwa mngeloyo n’kumuuza kuti andipatse mpukutu waung’onowo. Iye anandiuza kuti: “Tenga mpukutuwu udye.+ Ukupweteketsa m’mimba, koma m’kamwa mwako ukhala wozuna ngati uchi.”
8 “Iwe mwana wa munthu, imva zimene ndikukuuza. Usapanduke ngati nyumba yopandukayi.+ Tsegula pakamwa pako kuti udye zimene ndikukupatsa.”+
9 Choncho, ndinapita kwa mngeloyo n’kumuuza kuti andipatse mpukutu waung’onowo. Iye anandiuza kuti: “Tenga mpukutuwu udye.+ Ukupweteketsa m’mimba, koma m’kamwa mwako ukhala wozuna ngati uchi.”