-
2 Mbiri 18:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Poyankha, mfumu ya Isiraeli inauza Yehosafati+ kuti: “Pali munthu mmodzi+ amene tingathe kufunsira kwa Yehova kudzera mwa iye, koma ineyo ndimadana naye+ kwambiri, chifukwa masiku ake onse salosera zabwino zokhudza ine, koma zoipa zokhazokha.+ Munthuyo dzina lake ndi Mikaya mwana wa Imula.”+ Koma Yehosafati anati: “Musalankhule choncho mfumu.”+
-