Yesaya 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 amene auza anthu oona masomphenya kuti: ‘Lekani kuona masomphenya,’ ndipo anthu olosera zam’tsogolo awauza kuti: ‘Musamalosere zoona zokhudza ife.+ Muzilankhula kwa ife zabwino zokhazokha. Muziona masomphenya abodza.+ Amosi 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “‘Koma inu munapitiriza kupatsa Anaziri vinyo kuti amwe+ ndipo aneneri munawalamula kuti: “Musamanenere.”+ Amosi 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano mvera mawu a Yehova, ‘Kodi iwe ukundiuza kuti: “Usanenere zinthu zoipa zokhudza Isiraeli,+ ndipo usatchule mawu alionse oipa+ okhudza nyumba ya Isaki”?
10 amene auza anthu oona masomphenya kuti: ‘Lekani kuona masomphenya,’ ndipo anthu olosera zam’tsogolo awauza kuti: ‘Musamalosere zoona zokhudza ife.+ Muzilankhula kwa ife zabwino zokhazokha. Muziona masomphenya abodza.+
12 “‘Koma inu munapitiriza kupatsa Anaziri vinyo kuti amwe+ ndipo aneneri munawalamula kuti: “Musamanenere.”+
16 Tsopano mvera mawu a Yehova, ‘Kodi iwe ukundiuza kuti: “Usanenere zinthu zoipa zokhudza Isiraeli,+ ndipo usatchule mawu alionse oipa+ okhudza nyumba ya Isaki”?