Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 30:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 amene auza anthu oona masomphenya kuti: ‘Lekani kuona masomphenya,’ ndipo anthu olosera zam’tsogolo awauza kuti: ‘Musamalosere zoona zokhudza ife.+ Muzilankhula kwa ife zabwino zokhazokha. Muziona masomphenya abodza.+

  • Yeremiya 11:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Choncho Yehova wanena motsutsana ndi anthu a ku Anatoti+ amene akufuna moyo wako, ndipo akunena kuti: “Usanenere m’dzina la Yehova,+ ngati ukufuna kuti tisakuphe.”

  • Amosi 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndiyeno Amaziya anauza Amosi kuti: “Iwe wamasomphenya,+ choka, thawira kudziko la Yuda, ndipo kumeneko uzikadya mkate ndi kunenera.

  • Machitidwe 4:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Atatero anawaitana ndi kuwalamula kuti asalankhulenso kapena kuphunzitsa m’dzina la Yesu kwina kulikonse.

  • 1 Atesalonika 2:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Akutero pamene akuyesa kutiletsa+ kulankhula kwa anthu a mitundu ina kuti angapulumutsidwe.+ Chotsatira chake n’chakuti, pochita zimenezi nthawi zonse akudzazitsa+ machimo awo. Koma tsopano mkwiyo wake wawafikira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena