Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 23:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mobwerezabwereza iwo akuuza anthu amene sakundilemekeza kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Anthu inu mudzakhala pa mtendere.”’+ Ndipo aliyense woumitsa mtima wake+ akumuuza kuti, ‘Tsoka silidzakugwerani anthu inu.’+

  • Ezekieli 13:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Amuna inu, kodi masomphenya mwaonawa si abodza? Kodi zimene mwaloserazi si zonama? Inu mwati, ‘Yehova wanena kuti,’ pamene ine sindinalankhule kalikonse.”’+

  • Mika 2:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Munthu wolondola zinthu zopanda pake ndi zachinyengo akanena bodza lakuti:+ “Ndidzakulosererani zokhudza vinyo ndi chakumwa choledzeretsa,” ndiye adzakhale mneneri wa anthu awa.+

  • 2 Timoteyo 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pakuti idzafika nthawi imene anthu sadzafunanso chiphunzitso cholondola,+ koma mogwirizana ndi zilakolako zawo, adzadzipezera aphunzitsi kuti amve zowakomera m’khutu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena