Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 4:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pamenepo ndinanena kuti: “Kalanga ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Kunena zoona, mwapusitsa anthu awa+ ndiponso Yerusalemu mwa kunena kuti, ‘Mudzakhala pa mtendere,’+ koma lupanga lawabaya* mpaka mumtima.”

  • Yeremiya 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Iwo akuyesa kuchiritsa mwachinyengo+ kuwonongeka kwa anthu anga ponena kuti, ‘Kuli mtendere! Kuli mtendere!’ pamene kulibe mtendere.+

  • Yeremiya 8:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iwo akuyesa kuchiritsa mwachinyengo+ kuwonongeka kwa mwana wamkazi wa anthu anga ponena kuti: “Kuli mtendere! Kuli mtendere!” pamene kulibe mtendere.+

  • Ezekieli 13:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 chifukwa chakuti iwo asocheretsa anthu anga ponena kuti, “Tili pa mtendere!” Koma palibe mtendere.+ Palinso munthu amene akumanga khoma lachipinda, ndipo anthu ena akulipaka laimu pachabe.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena