Ezekieli 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zonsezi zidzachitika chifukwa chakuti iwo asocheretsa anthu anga ponena kuti, “Tili pa mtendere!” koma palibe mtendere.+ Munthu akamanga khoma lachipinda losalimba, iwo akumalipaka laimu.’*+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:10 Nsanja ya Olonda,10/1/1999, ptsa. 13-149/15/1988, tsa. 17
10 Zonsezi zidzachitika chifukwa chakuti iwo asocheretsa anthu anga ponena kuti, “Tili pa mtendere!” koma palibe mtendere.+ Munthu akamanga khoma lachipinda losalimba, iwo akumalipaka laimu.’*+