Yeremiya 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mobwerezabwereza iwo akuuza anthu amene sakundilemekeza kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Anthu inu mudzakhala pa mtendere.”’+ Ndipo aliyense woumitsa mtima wake+ akumuuza kuti, ‘Tsoka silidzakugwerani anthu inu.’+ Ezekieli 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 chifukwa chakuti iwo asocheretsa anthu anga ponena kuti, “Tili pa mtendere!” Koma palibe mtendere.+ Palinso munthu amene akumanga khoma lachipinda, ndipo anthu ena akulipaka laimu pachabe.’+
17 Mobwerezabwereza iwo akuuza anthu amene sakundilemekeza kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Anthu inu mudzakhala pa mtendere.”’+ Ndipo aliyense woumitsa mtima wake+ akumuuza kuti, ‘Tsoka silidzakugwerani anthu inu.’+
10 chifukwa chakuti iwo asocheretsa anthu anga ponena kuti, “Tili pa mtendere!” Koma palibe mtendere.+ Palinso munthu amene akumanga khoma lachipinda, ndipo anthu ena akulipaka laimu pachabe.’+