Yeremiya 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mobwerezabwereza iwo akuuza anthu amene sakundilemekeza kuti,‘Yehova wanena kuti: “Inu mudzakhala pa mtendere.”’+ Ndipo aliyense amene amatsatira mtima wake woipawo akumuuza kuti,‘Tsoka silidzakugwerani.’+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 23:17 Nsanja ya Olonda,3/1/1994, tsa. 11
17 Mobwerezabwereza iwo akuuza anthu amene sakundilemekeza kuti,‘Yehova wanena kuti: “Inu mudzakhala pa mtendere.”’+ Ndipo aliyense amene amatsatira mtima wake woipawo akumuuza kuti,‘Tsoka silidzakugwerani.’+