Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 18:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Munthu amene anatumidwa kukaitana Mikaya anauza Mikayayo kuti: “Tamvera, mawu amene aneneri onse alankhula kwa mfumu ndi abwino. Nawenso mawu ako akakhale ngati mawu awo,+ ndipo ukalankhule zabwino.”+

  • Salimo 127:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 127 Yehova akapanda kumanga nyumba,+

      Omanga nyumbayo amagwira ntchito pachabe.+

      Yehova akapanda kulondera mzinda,+

      Alonda amakhala maso pachabe.+

  • Yesaya 30:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 amene auza anthu oona masomphenya kuti: ‘Lekani kuona masomphenya,’ ndipo anthu olosera zam’tsogolo awauza kuti: ‘Musamalosere zoona zokhudza ife.+ Muzilankhula kwa ife zabwino zokhazokha. Muziona masomphenya abodza.+

  • Ezekieli 22:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Aneneri a mumzindawo apaka laimu machimo a atsogoleriwo.+ Aona masomphenya onama+ ndipo akuloserera atsogoleriwo zinthu zabodza.+ Iwo akunena kuti: “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti,” pamene Yehova sananene chilichonse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena