Ezekieli 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 chifukwa chakuti olosera anu anakuuzani masomphenya abodza,+ chifukwa chakuti anakulosererani zabodza, kuti mukhale pagulu la anthu ophedwa, anthu oipa amene tsiku lawo loti alangidwe lafika. Mapeto a zolakwa zawo zonse afika.+
29 chifukwa chakuti olosera anu anakuuzani masomphenya abodza,+ chifukwa chakuti anakulosererani zabodza, kuti mukhale pagulu la anthu ophedwa, anthu oipa amene tsiku lawo loti alangidwe lafika. Mapeto a zolakwa zawo zonse afika.+