Ezekieli 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakati pa nyumba ya Isiraeli sipadzakhalanso masomphenya opanda pake+ kapena kulosera kwachiphamaso.+ Ezekieli 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Aneneri a mumzindawo apaka laimu machimo a atsogoleriwo.+ Aona masomphenya onama+ ndipo akuloserera atsogoleriwo zinthu zabodza.+ Iwo akunena kuti: “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti,” pamene Yehova sananene chilichonse.
24 Pakati pa nyumba ya Isiraeli sipadzakhalanso masomphenya opanda pake+ kapena kulosera kwachiphamaso.+
28 Aneneri a mumzindawo apaka laimu machimo a atsogoleriwo.+ Aona masomphenya onama+ ndipo akuloserera atsogoleriwo zinthu zabodza.+ Iwo akunena kuti: “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti,” pamene Yehova sananene chilichonse.