Ezekieli 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 akazi inu simupitiriza kuona masomphenya abodza+ ndipo simudzaloseranso zam’tsogolo.+ Ineyo ndidzapulumutsa anthu anga m’manja mwanu+ ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”+
23 akazi inu simupitiriza kuona masomphenya abodza+ ndipo simudzaloseranso zam’tsogolo.+ Ineyo ndidzapulumutsa anthu anga m’manja mwanu+ ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”+