Ezekieli 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ine ndidzamuyang’ana mokwiya+ n’kumuika kuti akhale chenjezo+ ndi mwambi.+ Ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu anga,+ ndipo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’+
8 Ine ndidzamuyang’ana mokwiya+ n’kumuika kuti akhale chenjezo+ ndi mwambi.+ Ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu anga,+ ndipo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’+