Levitiko 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Munthu aliyense wa nyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzam’kana*+ ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake. Yeremiya 44:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Choncho Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndakukanani* ndipo ndikugwetserani tsoka ndi kupha anthu onse a mu Yuda.+ Ezekieli 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthuwo ndawayang’ana mokwiya.+ Iwo achoka pamoto, koma motowo uwanyeketsa.+ Anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, ndikadzawayang’ana mokwiya.’”+
10 “‘Munthu aliyense wa nyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzam’kana*+ ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.
11 “Choncho Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndakukanani* ndipo ndikugwetserani tsoka ndi kupha anthu onse a mu Yuda.+
7 Anthuwo ndawayang’ana mokwiya.+ Iwo achoka pamoto, koma motowo uwanyeketsa.+ Anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, ndikadzawayang’ana mokwiya.’”+