Ezekieli 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthuwo ndawayangʼana mokwiya. Iwo athawa moto, koma moto wina udzawapsereza. Ndipo ndikadzawayangʼana mokwiya, mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.+
7 Anthuwo ndawayangʼana mokwiya. Iwo athawa moto, koma moto wina udzawapsereza. Ndipo ndikadzawayangʼana mokwiya, mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.+