Numeri 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zitatero, nthaka inayasama n’kuwameza.+ Koma Kora anafa pamene moto unanyeketsa gulu la amuna 250.+ Choncho iwowa anakhala chitsanzo chopereka chenjezo.+
10 Zitatero, nthaka inayasama n’kuwameza.+ Koma Kora anafa pamene moto unanyeketsa gulu la amuna 250.+ Choncho iwowa anakhala chitsanzo chopereka chenjezo.+