Ezekieli 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho akazi inu simudzaonanso masomphenya abodza ndipo simudzaloseranso zamʼtsogolo.+ Ine ndidzapulumutsa anthu anga mʼmanja mwanu ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”
23 Choncho akazi inu simudzaonanso masomphenya abodza ndipo simudzaloseranso zamʼtsogolo.+ Ine ndidzapulumutsa anthu anga mʼmanja mwanu ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”