Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 18:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakati panu pasapezeke munthu wowotcha mwana wake pamoto,*+ wolosera,+ aliyense wochita zamatsenga,+ aliyense woombeza,+ wanyanga,+

  • Deuteronomo 18:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mitundu imene mukuilanda dziko inkamvera anthu ochita zamatsenga+ ndi olosera.+ Koma Yehova Mulungu wanu sanakuloleni kuti muzichita zimenezi.

  • Yeremiya 27:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 ‘Choncho musamvere aneneri, anthu ochita zamaula, olota maloto, ochita zamatsenga ndi obwebweta amene ali pakati panu ndipo akukuuzani kuti: “Simudzatumikira mfumu ya Babulo.”

  • Mika 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 ‘Usiku udzakufikirani,+ koma simudzaona masomphenya.+

      Kuzidzakhala mdima, koma inu simudzaloseranso.

      Aneneri amenewa dzuwa lidzawalowera.

      Ndipo mdima udzawagwera masanasana.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena