1 Mafumu 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu amene anatumidwa kukaitana Mikaya anauza Mikayayo kuti: “Tamvera, mawu amene aneneri onse alankhula kwa mfumu ndi abwino. Nawenso mawu ako akakhale ngati mawu a mmodzi wa iwo, ndipo ukalankhule zabwino.”+
13 Munthu amene anatumidwa kukaitana Mikaya anauza Mikayayo kuti: “Tamvera, mawu amene aneneri onse alankhula kwa mfumu ndi abwino. Nawenso mawu ako akakhale ngati mawu a mmodzi wa iwo, ndipo ukalankhule zabwino.”+