2 Mbiri 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu amene anatumidwa kukaitana Mikaya anauza Mikayayo kuti: “Tamvera, mawu amene aneneri onse alankhula kwa mfumu ndi abwino. Nawenso mawu ako akakhale ngati mawu awo,+ ndipo ukalankhule zabwino.”+
12 Munthu amene anatumidwa kukaitana Mikaya anauza Mikayayo kuti: “Tamvera, mawu amene aneneri onse alankhula kwa mfumu ndi abwino. Nawenso mawu ako akakhale ngati mawu awo,+ ndipo ukalankhule zabwino.”+