Salimo 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mumtima mwake+ amanena kuti: “Mulungu waiwala zochita zanga.+Wabisa nkhope yake.+Ndithudi, sadzaona kalikonse.”+ Yesaya 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 amene auza anthu oona masomphenya kuti: ‘Lekani kuona masomphenya,’ ndipo anthu olosera zam’tsogolo awauza kuti: ‘Musamalosere zoona zokhudza ife.+ Muzilankhula kwa ife zabwino zokhazokha. Muziona masomphenya abodza.+ Hoseya 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo amasangalatsa mfumu ndi zoipa zawo, ndiponso amasangalatsa akalonga ndi chinyengo chawo.+
11 Mumtima mwake+ amanena kuti: “Mulungu waiwala zochita zanga.+Wabisa nkhope yake.+Ndithudi, sadzaona kalikonse.”+
10 amene auza anthu oona masomphenya kuti: ‘Lekani kuona masomphenya,’ ndipo anthu olosera zam’tsogolo awauza kuti: ‘Musamalosere zoona zokhudza ife.+ Muzilankhula kwa ife zabwino zokhazokha. Muziona masomphenya abodza.+