Salimo 64:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Amaumirira kulankhula zoipa,+Amakambirana kuti atchere misampha.+Iwo amati: “Angaione ndani?”+ Mlaliki 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Popeza anthu ochita zoipa sanalangidwe msanga,+ n’chifukwa chake mtima wa ana a anthu wakhazikika pa kuchita zoipa.+
11 Popeza anthu ochita zoipa sanalangidwe msanga,+ n’chifukwa chake mtima wa ana a anthu wakhazikika pa kuchita zoipa.+