Mlaliki 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa anthu ochita zoipa sanalangidwe mwamsanga,+ anthu atsimikiza mtima kuchita zoipa.+ Mlaliki Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:11 Nsanja ya Olonda,9/1/2010, tsa. 4 Mtendere Weniweni, tsa. 135