Ekisodo 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Farao ataona kuti mliri wa achulewo watha, anaumitsa mtima wake,+ ndipo sanamvere Mose ndi Aroni, monga momwe Yehova ananenera.+ 1 Samueli 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndipo iye anali kuwauza kuti:+ “Mukuchitiranji zinthu zoterezi?+ Chifukwatu anthu onse akundiuza zinthu zoipa zokhazokha zokhudza inu.+ Salimo 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mumtima mwake amanena kuti: “Sindidzagwedezeka.+Palibe chimene chidzandichitikira ku mibadwomibadwo.”+ Yesaya 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngakhale munthu woipa atachitiridwa zabwino, sangaphunzire chilungamo.+ M’dziko lochita zowongoka, iye adzachita zinthu zopanda chilungamo+ ndipo sadzaona ukulu wa Yehova.+ Mateyu 24:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 “Koma ngati kapolo woipayo anganene mumtima mwake+ kuti, ‘Mbuye wanga akuchedwa,’+
15 Farao ataona kuti mliri wa achulewo watha, anaumitsa mtima wake,+ ndipo sanamvere Mose ndi Aroni, monga momwe Yehova ananenera.+
23 Ndipo iye anali kuwauza kuti:+ “Mukuchitiranji zinthu zoterezi?+ Chifukwatu anthu onse akundiuza zinthu zoipa zokhazokha zokhudza inu.+
6 Mumtima mwake amanena kuti: “Sindidzagwedezeka.+Palibe chimene chidzandichitikira ku mibadwomibadwo.”+
10 Ngakhale munthu woipa atachitiridwa zabwino, sangaphunzire chilungamo.+ M’dziko lochita zowongoka, iye adzachita zinthu zopanda chilungamo+ ndipo sadzaona ukulu wa Yehova.+