Ekisodo 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Farao ataona kuti mliri wa achulewo watha, anaumitsa mtima wake,+ ndipo sanamvere Mose ndi Aroni, monga momwe Yehova ananenera.+ Salimo 106:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Nthawi zambiri anali kuwalanditsa,+Koma iwo anali kumupandukira chifukwa sanali kumumvera,+Ndipo anali kuwatsitsa chifukwa cha zolakwa zawo.+ Miyambo 1:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pakuti kupanduka+ kwa osadziwa n’kumene kudzawaphe+ ndipo mphwayi za opusa n’zimene zidzawawononge.+
15 Farao ataona kuti mliri wa achulewo watha, anaumitsa mtima wake,+ ndipo sanamvere Mose ndi Aroni, monga momwe Yehova ananenera.+
43 Nthawi zambiri anali kuwalanditsa,+Koma iwo anali kumupandukira chifukwa sanali kumumvera,+Ndipo anali kuwatsitsa chifukwa cha zolakwa zawo.+
32 Pakuti kupanduka+ kwa osadziwa n’kumene kudzawaphe+ ndipo mphwayi za opusa n’zimene zidzawawononge.+