Yeremiya 48:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Anthu a ku Mowabu akhala mosatekeseka kuyambira pa unyamata wawo+ ndipo akukhalabe mosatekeseka ngati vinyo wansenga.+ Iwo sanatsanulidwepo kuchoka m’chiwiya china kupita m’chiwiya china ndipo sanapitepo ku ukapolo. N’chifukwa chake kukoma kwawo sikunawonjezeke ndipo fungo lawo silinasinthe. Chivumbulutso 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “‘Choncho, kumbukira malo amene unali usanagwe, lapa+ ndi kuchita ntchito za poyamba. Ngati sutero, ndikubwera kwa iwe,+ ndipo ndidzachotsa choikapo nyale chako+ pamalo ake ngati sulapa.
11 “Anthu a ku Mowabu akhala mosatekeseka kuyambira pa unyamata wawo+ ndipo akukhalabe mosatekeseka ngati vinyo wansenga.+ Iwo sanatsanulidwepo kuchoka m’chiwiya china kupita m’chiwiya china ndipo sanapitepo ku ukapolo. N’chifukwa chake kukoma kwawo sikunawonjezeke ndipo fungo lawo silinasinthe.
5 “‘Choncho, kumbukira malo amene unali usanagwe, lapa+ ndi kuchita ntchito za poyamba. Ngati sutero, ndikubwera kwa iwe,+ ndipo ndidzachotsa choikapo nyale chako+ pamalo ake ngati sulapa.