Salimo 123:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Moyo wathu wasautsika kwambiri chifukwa cha kunyoza kwa anthu amene akukhala mosatekeseka,+Ndiponso chifukwa cha kunyoza kwa anthu odzikuza.+ Miyambo 1:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Pakuti kupanduka+ kwa osadziwa n’kumene kudzawaphe+ ndipo mphwayi za opusa n’zimene zidzawawononge.+
4 Moyo wathu wasautsika kwambiri chifukwa cha kunyoza kwa anthu amene akukhala mosatekeseka,+Ndiponso chifukwa cha kunyoza kwa anthu odzikuza.+
32 Pakuti kupanduka+ kwa osadziwa n’kumene kudzawaphe+ ndipo mphwayi za opusa n’zimene zidzawawononge.+