Salimo 73:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Onani! Awa ndi anthu oipa, amene akukhala mosatekeseka mpaka kalekale.+Iwo achulukitsa chuma chawo.+ Salimo 119:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Anthu odzikuza andinyoza koopsa.+Koma ine sindinapatuke pa chilamulo chanu.+ Yeremiya 48:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Anthu a ku Mowabu akhala mosatekeseka kuyambira pa unyamata wawo+ ndipo akukhalabe mosatekeseka ngati vinyo wansenga.+ Iwo sanatsanulidwepo kuchoka m’chiwiya china kupita m’chiwiya china ndipo sanapitepo ku ukapolo. N’chifukwa chake kukoma kwawo sikunawonjezeke ndipo fungo lawo silinasinthe.
12 Onani! Awa ndi anthu oipa, amene akukhala mosatekeseka mpaka kalekale.+Iwo achulukitsa chuma chawo.+
11 “Anthu a ku Mowabu akhala mosatekeseka kuyambira pa unyamata wawo+ ndipo akukhalabe mosatekeseka ngati vinyo wansenga.+ Iwo sanatsanulidwepo kuchoka m’chiwiya china kupita m’chiwiya china ndipo sanapitepo ku ukapolo. N’chifukwa chake kukoma kwawo sikunawonjezeke ndipo fungo lawo silinasinthe.