Salimo 73:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Choncho kudzikuza kuli ngati mkanda m’khosi mwawo,+Ndipo avala chiwawa ngati malaya.+ Yeremiya 48:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Tamva za kunyada kwa Mowabu.+ Iye ndi wodzikuza kwambiri. Tamva za kudzikweza kwake, kunyada kwake, kudzikuza kwake ndi kudzitukumula kwa mtima wake.”+ 1 Akorinto 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ponyozedwa, timayankha mofatsa.+ Mpaka tsopano, takhala ngati zinyalala za dziko, nyansi za zinthu zonse.+
29 “Tamva za kunyada kwa Mowabu.+ Iye ndi wodzikuza kwambiri. Tamva za kudzikweza kwake, kunyada kwake, kudzikuza kwake ndi kudzitukumula kwa mtima wake.”+
13 Ponyozedwa, timayankha mofatsa.+ Mpaka tsopano, takhala ngati zinyalala za dziko, nyansi za zinthu zonse.+