Salimo 109:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye anali kuvala matemberero ngati chovala.+Matembererowo analowa mwa iye ngati madzi,+Ndiponso analowa m’mafupa ake ngati mafuta. Miyambo 3:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Usasirire munthu wachiwawa,+ kapena kusankha njira zake.+ Yakobo 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mwaweruza ndi kupha munthu wolungama. Iye akukutsutsani.+
18 Iye anali kuvala matemberero ngati chovala.+Matembererowo analowa mwa iye ngati madzi,+Ndiponso analowa m’mafupa ake ngati mafuta.