Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 37:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Usapse mtima chifukwa cha anthu ochita zoipa.+

      Usakhumbe kukhala ngati anthu ochita zosalungama.+

  • Miyambo 23:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Mtima wako usamasirire anthu ochimwa,+ koma iwe uziopa Yehova tsiku lonse.+

  • Miyambo 24:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Usamasirire anthu oipa,+ ndipo usamasonyeze kuti ukusirira kukhala pagulu lawo,+

  • Miyambo 24:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Usamapse mtima chifukwa cha anthu ochita zoipa. Usamasirire anthu oipa,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena