Salimo 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndimadana ndi mpingo wa anthu ochita zoipa,+Ndipo sindikhala pansi ndi anthu oipa.+ Salimo 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musandikokolole pamodzi ndi anthu oipa komanso anthu amene amachita zopweteka anzawo,+Anthu amene amalankhula mawu amtendere ndi anzawo+ koma m’mitima yawo muli zinthu zoipa.+ Miyambo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwana wanga, ochimwa akayesa kukunyengerera usavomere.+
3 Musandikokolole pamodzi ndi anthu oipa komanso anthu amene amachita zopweteka anzawo,+Anthu amene amalankhula mawu amtendere ndi anzawo+ koma m’mitima yawo muli zinthu zoipa.+