Salimo 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Taonani! Wina ali ndi pakati pa zinthu zoipa,+Watenga pakati pa mavuto ndipo ndithu adzabereka chinyengo.+ Salimo 36:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ali pabedi lake amakonza chiwembu kuti apweteke anzake.+Amaima panjira yoipa.+Sapewa kuchita zinthu zoipa.+ Miyambo 26:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ngakhale azilankhula mawu okoma,+ usam’khulupirire+ chifukwa mumtima mwake muli zinthu 7 zonyansa.+
14 Taonani! Wina ali ndi pakati pa zinthu zoipa,+Watenga pakati pa mavuto ndipo ndithu adzabereka chinyengo.+
4 Ali pabedi lake amakonza chiwembu kuti apweteke anzake.+Amaima panjira yoipa.+Sapewa kuchita zinthu zoipa.+
25 Ngakhale azilankhula mawu okoma,+ usam’khulupirire+ chifukwa mumtima mwake muli zinthu 7 zonyansa.+