2 Samueli 13:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamapeto pake Abisalomu anati: “Ngati inuyo simubwera, chonde lolani kuti Aminoni m’bale wanga apite nafe.”+ Pamenepo mfumu inamufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani ukufuna kuti apite nawe?” Salimo 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo amalankhulana zabodza.+Amalankhulana ndi milomo yoshashalika+ komanso ndi mitima iwiri.+ Salimo 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musandikokolole pamodzi ndi anthu oipa komanso anthu amene amachita zopweteka anzawo,+Anthu amene amalankhula mawu amtendere ndi anzawo+ koma m’mitima yawo muli zinthu zoipa.+
26 Pamapeto pake Abisalomu anati: “Ngati inuyo simubwera, chonde lolani kuti Aminoni m’bale wanga apite nafe.”+ Pamenepo mfumu inamufunsa kuti: “N’chifukwa chiyani ukufuna kuti apite nawe?”
3 Musandikokolole pamodzi ndi anthu oipa komanso anthu amene amachita zopweteka anzawo,+Anthu amene amalankhula mawu amtendere ndi anzawo+ koma m’mitima yawo muli zinthu zoipa.+