1 Mbiri 12:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 A fuko la Zebuloni,+ onse oyenerera kupita kunkhondo, kukafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo ndi zida zawo zonse zankhondo, analipo 50,000. Popita kwa Davide, iwo sanapite ndi mitima iwiri.
33 A fuko la Zebuloni,+ onse oyenerera kupita kunkhondo, kukafola mwa dongosolo lomenyera nkhondo ndi zida zawo zonse zankhondo, analipo 50,000. Popita kwa Davide, iwo sanapite ndi mitima iwiri.