Salimo 55:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mawu a pakamwa pake ndi osalala ngati mafuta a mkaka,+Koma mtima wake umakonda ndewu.+Mawu ake ndi osalala ngati mafuta,+Koma ali ngati lupanga lakuthwa.+ Miyambo 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene pali munthu wobisa chidani pamakhala milomo yonyenga,+ ndipo wobweretsa uthenga woipa ndi wopusa.+ Miyambo 26:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu wodana nawe amadzibisa ndi milomo yake, koma mkati mwake mumakhala chinyengo.+
21 Mawu a pakamwa pake ndi osalala ngati mafuta a mkaka,+Koma mtima wake umakonda ndewu.+Mawu ake ndi osalala ngati mafuta,+Koma ali ngati lupanga lakuthwa.+
18 Pamene pali munthu wobisa chidani pamakhala milomo yonyenga,+ ndipo wobweretsa uthenga woipa ndi wopusa.+