2 Samueli 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Abisalomu sanalankhule chilichonse, chabwino kapena choipa kwa m’bale wake Aminoni, pakuti Abisalomu anadana+ ndi Aminoni chifukwa chochititsa manyazi Tamara mlongo wake. Miyambo 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamene pali munthu wobisa chidani pamakhala milomo yonyenga,+ ndipo wobweretsa uthenga woipa ndi wopusa.+
22 Abisalomu sanalankhule chilichonse, chabwino kapena choipa kwa m’bale wake Aminoni, pakuti Abisalomu anadana+ ndi Aminoni chifukwa chochititsa manyazi Tamara mlongo wake.
18 Pamene pali munthu wobisa chidani pamakhala milomo yonyenga,+ ndipo wobweretsa uthenga woipa ndi wopusa.+