Salimo 59:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Taonani! Amabwetuka ndi pakamwa pawo.+Milomo yawo ili ngati malupanga,+Pakuti iwo amati: “Ndani akumvetsera?”+ Miyambo 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pali munthu amene amalankhula mosaganizira ndi mawu olasa ngati lupanga,+ koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+
7 Taonani! Amabwetuka ndi pakamwa pawo.+Milomo yawo ili ngati malupanga,+Pakuti iwo amati: “Ndani akumvetsera?”+
18 Pali munthu amene amalankhula mosaganizira ndi mawu olasa ngati lupanga,+ koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+