Salimo 57:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Moyo wanga uli pakati pa mikango.+Sindingachitire mwina koma kugona pakati pa ana a anthu, amene ali ngati nyama zoopsa zodya anthu,Amene mano awo ali ngati mikondo ndi mivi,+Ndipo lilime lawo lili ngati lupanga lakuthwa.+ Salimo 64:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amene anola lilime lawo ngati lupanga,+Amene alunjikitsa mivi yawo, imene ndi mawu awo owawa,+ Miyambo 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pali munthu amene amalankhula mosaganizira ndi mawu olasa ngati lupanga,+ koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+
4 Moyo wanga uli pakati pa mikango.+Sindingachitire mwina koma kugona pakati pa ana a anthu, amene ali ngati nyama zoopsa zodya anthu,Amene mano awo ali ngati mikondo ndi mivi,+Ndipo lilime lawo lili ngati lupanga lakuthwa.+
3 Amene anola lilime lawo ngati lupanga,+Amene alunjikitsa mivi yawo, imene ndi mawu awo owawa,+ Miyambo 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pali munthu amene amalankhula mosaganizira ndi mawu olasa ngati lupanga,+ koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+
18 Pali munthu amene amalankhula mosaganizira ndi mawu olasa ngati lupanga,+ koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+