Salimo 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti oipa akunga uta,+Akonzekeretsa mivi yawo kuti aiponye ndi uta,Kuti alase anthu owongoka mtima kuchokera pamalo amdima.+ Salimo 58:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Asungunuke ndi kupita ngati madzi.+Mulungu akunge uta woponyera mivi yake pamene adaniwo akugwa.+ Yeremiya 9:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Lilime lawo ndiwo muvi wophera anthu.+ Limalankhula chinyengo chokhachokha. Munthu aliyense amalankhula mwamtendere ndi mnzake, koma mumtima mwake amakonza chiwembu.”+
2 Pakuti oipa akunga uta,+Akonzekeretsa mivi yawo kuti aiponye ndi uta,Kuti alase anthu owongoka mtima kuchokera pamalo amdima.+
8 Lilime lawo ndiwo muvi wophera anthu.+ Limalankhula chinyengo chokhachokha. Munthu aliyense amalankhula mwamtendere ndi mnzake, koma mumtima mwake amakonza chiwembu.”+