Salimo 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo amalankhulana zabodza.+Amalankhulana ndi milomo yoshashalika+ komanso ndi mitima iwiri.+ Salimo 120:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi iwe lilime lachinyengo,+Munthu adzakupatsa chiyani ndipo adzawonjezera chiyani pa iwe?