Salimo 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 M’kamwa mwake mwadzaza matemberero, chinyengo ndi kupondereza ena.+Pansi pa lilime lake pamatuluka mavuto ndi zopweteka ena.+ Salimo 41:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wina akabwera kudzandiona, amalankhula zabodza kuchokera mumtima mwake.+Amasonkhanitsa nkhani zoipa.Akatero amachoka, ndipo kunjako amauza ena zabodza zokhudza ine.+
7 M’kamwa mwake mwadzaza matemberero, chinyengo ndi kupondereza ena.+Pansi pa lilime lake pamatuluka mavuto ndi zopweteka ena.+
6 Wina akabwera kudzandiona, amalankhula zabodza kuchokera mumtima mwake.+Amasonkhanitsa nkhani zoipa.Akatero amachoka, ndipo kunjako amauza ena zabodza zokhudza ine.+