Salimo 52:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Umakonda mawu onse owononga,+Lilime lachinyengo iwe.+ Miyambo 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Milomo yonama imam’nyansa Yehova,+ koma anthu ochita zinthu mokhulupirika amam’sangalatsa.+ Yakobo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Lilimenso ndi moto.+ Mwa ziwalo zathu zonse, lilime ndilo lili lodzaza ndi zosalungama chifukwa limadetsa thupi lonse.+ Lili ndi moto wa Gehena* ndipo limayatsa moyo wonse wa munthu.
6 Lilimenso ndi moto.+ Mwa ziwalo zathu zonse, lilime ndilo lili lodzaza ndi zosalungama chifukwa limadetsa thupi lonse.+ Lili ndi moto wa Gehena* ndipo limayatsa moyo wonse wa munthu.