Salimo 120:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwe lilime lachinyengo,+Kodi Mulungu adzakuchitira chiyani ndipo adzakupatsa chilango chotani?*